Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+

      Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+

      Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+

  • 1 Samueli 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+

      Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+

  • 1 Mbiri 17:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Inu Yehova, palibe wofanana nanu,+ ndipo malinga ndi zonse zimene tamva ndi makutu athu, palibenso Mulungu wina koma inu nokha.+

  • Salimo 83:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+

      Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+

  • Salimo 89:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Pakuti ndani kumwamba angayerekezeredwe ndi Yehova?+

      Ndani angafanane ndi Yehova pakati pa ana a Mulungu?+

  • Yeremiya 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndithudi palibe aliyense wofanana ndi inu Yehova.+ Inu ndinu wamkulu, ndipo dzina lanu ndi lalikulu ndi lamphamvu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena