Oweruza 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo,+ n’kuyamba kutsatira milungu ina mwa milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milungu imeneyo, moti anakhumudwitsa Yehova.+ 1 Samueli 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zinthu zonse zimene akhala akuchita kuyambira pa tsiku limene ndinawatulutsa mu Iguputo+ mpaka lero, kundisiya+ n’kumakatumikira milungu ina,+ n’zimenenso akuchitira iwe. 2 Mbiri 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma inuyo mukadzabwerera+ n’kusiya kutsatira malamulo anga+ amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina+ ndi kuigwadira,+
12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo,+ n’kuyamba kutsatira milungu ina mwa milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milungu imeneyo, moti anakhumudwitsa Yehova.+
8 Zinthu zonse zimene akhala akuchita kuyambira pa tsiku limene ndinawatulutsa mu Iguputo+ mpaka lero, kundisiya+ n’kumakatumikira milungu ina,+ n’zimenenso akuchitira iwe.
19 Koma inuyo mukadzabwerera+ n’kusiya kutsatira malamulo anga+ amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina+ ndi kuigwadira,+