Salimo 69:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndanyamula chitonzo chifukwa cha inu,+Manyazi aphimba nkhope yanga.+ Mateyu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+ Aroma 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ngakhale Khristu sanadzikondweretse yekha,+ koma anachita mmene Malemba amanenera kuti: “Mnyozo wa anthu amene anali kukutonzani wagwa pa ine.”+
22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+
3 Pakuti ngakhale Khristu sanadzikondweretse yekha,+ koma anachita mmene Malemba amanenera kuti: “Mnyozo wa anthu amene anali kukutonzani wagwa pa ine.”+