-
Yobu 5:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Pakuti iye amayambitsa kupweteka, koma amamanga chilonda chopwetekacho.
Amaphwanya anthu, koma manja ake ndi amene amawachiritsa.
-