Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 30:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chitetezo cha Farao chidzakhala chochititsa manyazi kwa amuna inu,+ ndipo kubisala mumthunzi wa Iguputo kudzakhala chinthu chopereka chitonzo.+

  • Yesaya 31:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma Aiguputowo ndi anthu ochokera kufumbi.+ Si Mulungu ayi. Mahatchi awo ndi zinyama,+ osati mzimu. Yehova akadzatambasula dzanja lake, amene akupereka thandizo adzapunthwa, ndipo amene akuthandizidwawo adzagwa.+ Onsewo adzatha nthawi imodzi.

  • Yeremiya 37:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Anthu inu mukauze mfumu ya Yuda imene yakutumani kuno kudzafunsira uthenga wa Mulungu kwa ine+ kuti: “Taonani! Gulu lankhondo la Farao limene likubwera kwa anthu inu kuti likuthandizeni lidzabwerera kwawo ku Iguputo.+

  • Ezekieli 29:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu onse okhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova+ chifukwa chakuti iwo anali ngati bango loyendera la nyumba ya Isiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena