Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Pa nthawiyo, adzakhala atasiya dziko lawo, ndipo dzikolo lidzakhala likubweza masabata ake+ pamene lidzakhala bwinja iwowo kulibe. Iwo adzakhala akulipira chifukwa cha zolakwa zawo,+ chifukwa chakuti anakana zigamulo zanga+ ndipo ananyansidwa ndi malamulo anga.+

  • Yesaya 40:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Mulankhuleni Yerusalemu momufika pamtima.+ Muuzeni mofuula kuti ntchito yake yogwira mokakamizidwa yatha,+ ndiponso kuti zolakwa zake zalipiridwa.+ Pakuti kuchokera m’dzanja la Yehova, iye walandira malipiro okwanira a machimo ake onse.”+

  • Yeremiya 50:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “M’masiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo,+ cholakwa cha Isiraeli chidzafufuzidwa+ koma sichidzapezeka,” watero Yehova. “Machimo a Yuda+ adzafufuzidwa koma sadzapezeka, pakuti ine ndidzakhululukira anthu amene ndawasiya amoyo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena