1 Samueli 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kulingalira bwino kwako.+ Udalitsike chifukwa cha kundigwira lero kuti ndisapalamule mlandu wamagazi+ ndi kudzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.+ Machitidwe 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Choncho khalani maso, ndipo kumbukirani kuti kwa zaka zitatu,+ usana ndi usiku, sindinaleke kuchenjeza+ aliyense wa inu ndi misozi.
33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kulingalira bwino kwako.+ Udalitsike chifukwa cha kundigwira lero kuti ndisapalamule mlandu wamagazi+ ndi kudzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.+
31 “Choncho khalani maso, ndipo kumbukirani kuti kwa zaka zitatu,+ usana ndi usiku, sindinaleke kuchenjeza+ aliyense wa inu ndi misozi.