Levitiko 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzam’kana* munthu ameneyo, ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki kuti aipitse malo anga oyera+ ndi kuipitsa dzina langa loyera.+ Yeremiya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi nyumba iyi, imene yatchedwa ndi dzina langa,+ mwayamba kuiona ngati phanga la achifwamba?+ Inetu ndaona zimene mukuchita,” watero Yehova.+
3 Ine ndidzam’kana* munthu ameneyo, ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki kuti aipitse malo anga oyera+ ndi kuipitsa dzina langa loyera.+
11 Kodi nyumba iyi, imene yatchedwa ndi dzina langa,+ mwayamba kuiona ngati phanga la achifwamba?+ Inetu ndaona zimene mukuchita,” watero Yehova.+