Ezekieli 35:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uuze deralo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe dera lamapiri la Seiri,+ ine ndithana nawe. Nditambasula dzanja langa ndi kukukhaulitsa.+ Ndikusandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka.+ Zefaniya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndidzatambasula dzanja langa ndi kuwononga Yuda pamodzi ndi anthu onse okhala mu Yerusalemu.+ Ndidzawononga anthu onse otsala amene amapembedza Baala+ ndi kuwachotsa pamalo ano. Ndidzafafanizanso dzina la ansembe a mulungu wachilendo pamodzi ndi ansembe ena.+
3 Uuze deralo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe dera lamapiri la Seiri,+ ine ndithana nawe. Nditambasula dzanja langa ndi kukukhaulitsa.+ Ndikusandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka.+
4 “Ndidzatambasula dzanja langa ndi kuwononga Yuda pamodzi ndi anthu onse okhala mu Yerusalemu.+ Ndidzawononga anthu onse otsala amene amapembedza Baala+ ndi kuwachotsa pamalo ano. Ndidzafafanizanso dzina la ansembe a mulungu wachilendo pamodzi ndi ansembe ena.+