Ezekieli 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Zinthu zimene unasunga+ zikafika kumtunda+ zinali kukwanira mitundu yambiri ya anthu.+ Mafumu a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zako zochuluka zamtengo wapatali ndi katundu wako wogulitsa.+ 1 Timoteyo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+
33 Zinthu zimene unasunga+ zikafika kumtunda+ zinali kukwanira mitundu yambiri ya anthu.+ Mafumu a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zako zochuluka zamtengo wapatali ndi katundu wako wogulitsa.+
17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+