Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iwo adzakulanda chuma chako+ ndi malonda ako.+ Adzagwetsa mpanda wako ndi nyumba zako zosiririka. Miyala yako, zinthu zako zamatabwa ndi fumbi lako, adzaziponya m’madzi.’

  • Ezekieli 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “‘“Chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako,+ chifukwa cha malonda ako opanda chilungamo,+ waipitsa malo ako opatulika. Ndidzabweretsa moto kuchokera pakati pako, ndipo udzakunyeketsa.+ Ndidzakusandutsa phulusa padziko lapansi pamaso pa anthu onse okuona.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena