18 “‘“Chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako,+ chifukwa cha malonda ako opanda chilungamo,+ waipitsa malo ako opatulika. Ndidzabweretsa moto kuchokera pakati pako, ndipo udzakunyeketsa.+ Ndidzakusandutsa phulusa padziko lapansi pamaso pa anthu onse okuona.+