Yesaya 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mbewu za ku Sihori+ ndi zokolola za kumtsinje wa Nailo, zimene zinali kuyenda pamadzi ambiri ndiponso zimene zinali kukubweretserani ndalama, zakhala phindu la mitundu ina ya anthu.+ Ezekieli 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘“Tarisi+ unali kuchita naye malonda a zinthu zambiri zosiyanasiyana zamtengo wapatali.+ Unamupatsa zinthu zako zimene unasunga posinthanitsa ndi siliva, chitsulo, tini ndi mtovu.+
3 Mbewu za ku Sihori+ ndi zokolola za kumtsinje wa Nailo, zimene zinali kuyenda pamadzi ambiri ndiponso zimene zinali kukubweretserani ndalama, zakhala phindu la mitundu ina ya anthu.+
12 “‘“Tarisi+ unali kuchita naye malonda a zinthu zambiri zosiyanasiyana zamtengo wapatali.+ Unamupatsa zinthu zako zimene unasunga posinthanitsa ndi siliva, chitsulo, tini ndi mtovu.+