Ezekieli 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova wanena kuti, ‘Nawonso othandiza Iguputo adzaphedwa, ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.’+ “‘Kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,+ anthu adzaphedwa ndi lupanga m’dzikolo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
6 “Yehova wanena kuti, ‘Nawonso othandiza Iguputo adzaphedwa, ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.’+ “‘Kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,+ anthu adzaphedwa ndi lupanga m’dzikolo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.