Genesis 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yakobo anatsogoza amithenga+ ake powatumiza kwa Esau m’bale wake, kudziko la Seiri,+ kudera la Edomu.+ Deuteronomo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musalimbane nawo, chifukwa sindikupatsani dziko lawo, ngakhale kachigawo kokwana phazi limodzi lokha. Ndinapereka phiri la Seiri kwa Esau kuti likhale malo ake.+ Ezekieli 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+
3 Kenako Yakobo anatsogoza amithenga+ ake powatumiza kwa Esau m’bale wake, kudziko la Seiri,+ kudera la Edomu.+
5 Musalimbane nawo, chifukwa sindikupatsani dziko lawo, ngakhale kachigawo kokwana phazi limodzi lokha. Ndinapereka phiri la Seiri kwa Esau kuti likhale malo ake.+
8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+