8 Ndani anamvapo zinthu ngati zimenezi?+ Ndani anaonapo zinthu zoterezi?+ Kodi dziko+ limatulutsidwa ndi zowawa za pobereka tsiku limodzi lokha?+ Kapena kodi mtundu+ umabadwa nthawi imodzi?+ Pakuti Ziyoni wamva zowawa za pobereka ndipo wabereka ana ake aamuna.