2 Ine ndidzasonkhanitsanso pamodzi mitundu yonse ya anthu+ ndi kuibweretsa m’chigwa cha Yehosafati+ ndipo ndidzaiweruza chifukwa cha anthu anga ndi cholowa changa, Isiraeli.+ Mitundu imeneyi inamwaza Isiraeli pakati pa mitundu ya anthu ndiponso inagawana dziko langa.+