Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 26:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Yehova wanena kuti, ‘Ukaimirire m’bwalo la nyumba ya Yehova,+ ndipo anthu onse amene akubwera kudzalambira panyumba ya Yehova ukawauze zimene zidzachitikira mizinda yonse ya Yuda. Ukawauze mawu onse amene ndidzakulamula kuti uwauze.+ Usachotsepo mawu ngakhale amodzi.+

  • Ezekieli 43:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Koma iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli za Nyumba+ ino kuti achite manyazi chifukwa cha zolakwa zawo,+ ndipo adzayeze nyumbayi ndi kudziwa tsatanetsatane wa kamangidwe kake.

  • Machitidwe 20:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti sindinakubisireni kanthu, koma ndinakuuzani chifuniro+ chonse cha Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena