Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake,+ popeza ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.

  • Numeri 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Gawo limenelo lizikhala lako pazopereka zopatulika koposa, ndizo nsembe zonse zotentha ndi moto. Nsembezo, zimene azibwera nazo kwa ine, ndi izi: Nsembe zawo zambewu,+ nsembe zawo zamachimo,+ nsembe zawo za kupalamula,+ ndi nsembe zawo zina zonse. Gawolo lizikhala chinthu chopatulika koposa kwa iwe ndi ana ako.

  • Nehemiya 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Eliyasibu anakonzera Tobia chipinda chachikulu chodyeramo+ m’chipinda chimene nthawi zonse anali kuikamo nsembe yambewu,+ lubani,* ziwiya, chakhumi cha mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta+ zimene Alevi,+ oimba ndi alonda a pazipata anayenera kulandira, komanso zimene anali kupereka kwa ansembe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena