Genesis 31:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Pambuyo pake, Yakobo anapereka nsembe m’phirimo n’kuitana abale ake kuti adye chakudya.+ Motero iwo anadya chakudya n’kugona m’phirimo usiku umenewo. Deuteronomo 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani. 1 Akorinto 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taganizirani zochitika za Isiraeli wakuthupi:+ Kodi amene amadyako zoperekedwa nsembe sindiye kuti akugawana ndi guwa lansembe?+
54 Pambuyo pake, Yakobo anapereka nsembe m’phirimo n’kuitana abale ake kuti adye chakudya.+ Motero iwo anadya chakudya n’kugona m’phirimo usiku umenewo.
7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.
18 Taganizirani zochitika za Isiraeli wakuthupi:+ Kodi amene amadyako zoperekedwa nsembe sindiye kuti akugawana ndi guwa lansembe?+