45 “‘Anthu inu, pogawana dzikoli kuti likhale cholowa chanu,+ mudzapatule malo ena ndi kuwapereka kwa Yehova+ monga gawo loyera.+ M’litali mwa malo amenewo mudzakhale mikono 25,000, ndipo m’lifupi mudzakhale mikono 10,000.+ Malo onsewo adzakhale gawo loyera.