Salimo 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mudzawabisa m’malo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa pamaso pa anthu amene asonkhana pamodzi kuti awachitire chiwembu.+Mudzawabisa mumsasa wanu kwa anthu ofuna kukangana nawo.+ Salimo 90:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Inu Yehova, ndinudi malo athu okhalamo+Ku mibadwomibadwo.+ Salimo 91:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Popeza wanena kuti: “Yehova ndiye pothawirapo panga,”+Wapanga Wam’mwambamwamba kukhala malo ako okhalamo.+ Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+
20 Mudzawabisa m’malo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa pamaso pa anthu amene asonkhana pamodzi kuti awachitire chiwembu.+Mudzawabisa mumsasa wanu kwa anthu ofuna kukangana nawo.+
9 Popeza wanena kuti: “Yehova ndiye pothawirapo panga,”+Wapanga Wam’mwambamwamba kukhala malo ako okhalamo.+ Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+