Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Sikuti mukulowa m’dziko ili kukalitenga kukhala lanu chifukwa cha kulungama kwanu+ kapena chifukwa cha kuwongoka mtima kwanu.+ Yehova Mulungu wanu akukankhira mitundu iyi kutali ndi inu, kwenikweni chifukwa cha kuipa kwawo,+ ndiponso kuti Yehova akwaniritse mawu onse amene analumbirira makolo anu Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+

  • Deuteronomo 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa muyenera kuwawononga ndithu. Mukawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani.

  • Yoswa 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho mafumu asanu a Aamoriwo+ anakumana pamodzi n’kunyamuka. Mafumuwo anali: Mfumu ya ku Yerusalemu, mfumu ya ku Heburoni, mfumu ya ku Yarimuti, mfumu ya ku Lakisi, ndi mfumu ya ku Egiloni. Mafumu amenewa, pamodzi ndi magulu awo ankhondo anakamanga msasa pafupi ndi mzinda wa Gibeoni, n’cholinga chouthira nkhondo.

  • 2 Mafumu 21:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena