Yeremiya 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa m’manja mwa mtumiki wanga+ Nebukadinezara, mfumu ya Babulo.+ Ndamupatsanso nyama zakutchire kuti zimutumikire.+ Ezekieli 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zinali kumanga zisa zawo m’nthambi zake zikuluzikuluzo.+ Nyama zonse zakutchire zinkaberekera pansi pa nthambi zake.+ Mitundu yonse ya anthu ambiri inali kukhala mumthunzi wake.
6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa m’manja mwa mtumiki wanga+ Nebukadinezara, mfumu ya Babulo.+ Ndamupatsanso nyama zakutchire kuti zimutumikire.+
6 Zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zinali kumanga zisa zawo m’nthambi zake zikuluzikuluzo.+ Nyama zonse zakutchire zinkaberekera pansi pa nthambi zake.+ Mitundu yonse ya anthu ambiri inali kukhala mumthunzi wake.