Ezekieli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wafanana ndi Msuri. Wafanana ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wanthambi zikuluzikulu zokongola,+ wanthambi za masamba ambiri zopereka mthunzi, mtengo wautali kwambiri+ umene nsonga yake inafika m’mitambo.+ Danieli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Ine ndinaona masomphenya nditagona pabedi langa.+ Ndinaona mtengo+ wautali kwambiri+ uli pakati pa dziko lapansi.
3 Wafanana ndi Msuri. Wafanana ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wanthambi zikuluzikulu zokongola,+ wanthambi za masamba ambiri zopereka mthunzi, mtengo wautali kwambiri+ umene nsonga yake inafika m’mitambo.+
10 “‘Ine ndinaona masomphenya nditagona pabedi langa.+ Ndinaona mtengo+ wautali kwambiri+ uli pakati pa dziko lapansi.