Danieli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense amene sagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kulambira fanolo,+ nthawi yomweyo+ aponyedwa m’ng’anjo yoyaka moto.”+ Danieli 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene anali kuchita zimenezi, zala za munthu zinaonekera ndipo zinayamba kulemba pafupi ndi choikapo nyale, papulasitala wa pakhoma* la nyumba ya mfumu,+ ndipo mfumuyo inaona dzanja limene linali kulembalo.
6 Aliyense amene sagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kulambira fanolo,+ nthawi yomweyo+ aponyedwa m’ng’anjo yoyaka moto.”+
5 Pamene anali kuchita zimenezi, zala za munthu zinaonekera ndipo zinayamba kulemba pafupi ndi choikapo nyale, papulasitala wa pakhoma* la nyumba ya mfumu,+ ndipo mfumuyo inaona dzanja limene linali kulembalo.