Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 47:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano imirira, tenga nyanga zako ndiponso zamatsenga zako zambirimbiri+ zomwe wazivutikira kuyambira uli mwana. Uzitenge kuti mwina zingakuthandize kapenanso kuti ungachite nazo zodabwitsa kwa anthu.

  • Danieli 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Akasidiwo anayankha mfumuyo kuti: “Palibe munthu padziko lapansi amene angathe kuuza inu mfumu zimene mukufuna, pakuti palibe mfumu yaikulu kapena bwanamkubwa amene anauzapo wansembe wochita zamatsenga kapena munthu wolankhula ndi mizimu kapena Mkasidi kuti achite zimenezi.

  • Danieli 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pa nthawi imeneyo amuna onse anzeru anabwera kwa mfumu koma sanathe kuwerenga mawu olembedwawo kapena kuiuza mfumu kumasulira kwake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena