2 Mbiri 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ziwiya zina+ za m’nyumba ya Yehova, Nebukadinezara+ anapita nazo ku Babulo n’kukaziika m’nyumba yake yachifumu.+ Yeremiya 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Yehova wa makamu wanena mawu okhudza zipilala,+ thanki ya madzi,*+ zotengera zamawilo+ ndi ziwiya zotsala mumzinda uwu,+
7 Ziwiya zina+ za m’nyumba ya Yehova, Nebukadinezara+ anapita nazo ku Babulo n’kukaziika m’nyumba yake yachifumu.+
19 “Yehova wa makamu wanena mawu okhudza zipilala,+ thanki ya madzi,*+ zotengera zamawilo+ ndi ziwiya zotsala mumzinda uwu,+