Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anaumba zipilala ziwiri zamkuwa.+ Kutalika kwa chipilala chilichonse kunali mikono 18, ndipo pankafunika chingwe chotalika mikono 12 kuti ayeze kuzungulira chipilala chilichonse.+

  • 2 Mafumu 25:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chipilala chilichonse kutalika kwake chinali mikono 18,+ ndipo mutu+ wake unali wamkuwa. Mutuwo kutalika kwake kunali mikono itatu, ndipo maukonde ndi makangaza*+ amene anazungulira mutuwo, onse anali amkuwa. Chipilala chachiwiri chinalinso ndi maukonde ofanana ndi amenewa.

  • 2 Mbiri 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anapanga zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yozungulira+ imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo, ndiponso maukonde awiri+ okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pamwamba pa zipilalazo.

  • Yeremiya 52:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ponena za zipilalazo, chipilala chilichonse chinali chotalika mikono* 18,+ ndipo chinali kuzunguliridwa ndi chingwe chotalika mikono 12.+ Chipilala chilichonse chinali champhako ndipo kuchindikala kwake kunali kofanana ndi mphipi ya zala zinayi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena