Danieli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga,+ anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo.+ Anthu amenewa anafika ndi kuima pamaso pa mfumu. Danieli 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Chotero ansembe ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi*+ ndi okhulupirira nyenyezi+ anabwera kwa ine ndipo ndinawauza malotowo, koma iwo sanathe kuwamasulira.+ Danieli 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo amuna onse anzeru anabwera kwa mfumu koma sanathe kuwerenga mawu olembedwawo kapena kuiuza mfumu kumasulira kwake.+
2 Pamenepo mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga,+ anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo.+ Anthu amenewa anafika ndi kuima pamaso pa mfumu.
7 “Chotero ansembe ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi*+ ndi okhulupirira nyenyezi+ anabwera kwa ine ndipo ndinawauza malotowo, koma iwo sanathe kuwamasulira.+
8 Pa nthawi imeneyo amuna onse anzeru anabwera kwa mfumu koma sanathe kuwerenga mawu olembedwawo kapena kuiuza mfumu kumasulira kwake.+