Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+

  • Yeremiya 48:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 “Yehova wanena kuti, ‘Taonani! Monga mmene chiwombankhanga chimatsikira ndi kugwira chakudya chake,+ wina adzatambasula mapiko ake ndi kugwira Mowabu.+

  • Maliro 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Otithamangitsawo ndi aliwiro kuposa ziwombankhanga zouluka m’mwamba.+

      Iwo atithamangitsa pamapiri.+ Atibisalira m’chipululu.+

  • Habakuku 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mahatchi* ake ndi aliwiro kuposa akambuku* ndiponso ndi oopsa kuposa mimbulu yoyenda usiku.+ Mahatchi ake ankhondo amachita mgugu ndipo amachokera kutali. Mahatchiwo amauluka ngati chiwombankhanga chimene chikuthamangira chakudya chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena