Danieli 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikukutamandani ndi kukuyamikani,+ inu Mulungu wa makolo anga, chifukwa mwandipatsa nzeru+ ndi mphamvu. Tsopano mwandiuza zimene tinakupemphani, pakuti mwatidziwitsa zimene mfumu inali kufuna.”+ Danieli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: Danieli 2:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mfumuyo inauza Danieli kuti: “Ndithudi Mulungu wa anthu inu ndi Mulungu wa milungu yonse,+ Ambuye wa mafumu onse+ ndiponso Woulula zinsinsi, chifukwa iwe wakwanitsa kuulula chinsinsi chimenechi.”+
23 Ndikukutamandani ndi kukuyamikani,+ inu Mulungu wa makolo anga, chifukwa mwandipatsa nzeru+ ndi mphamvu. Tsopano mwandiuza zimene tinakupemphani, pakuti mwatidziwitsa zimene mfumu inali kufuna.”+
28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa:
47 Mfumuyo inauza Danieli kuti: “Ndithudi Mulungu wa anthu inu ndi Mulungu wa milungu yonse,+ Ambuye wa mafumu onse+ ndiponso Woulula zinsinsi, chifukwa iwe wakwanitsa kuulula chinsinsi chimenechi.”+