Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ana a Yafeti anali Gomeri,+ Magogi,+ Madai,+ Yavani,+ Tubala,+ Meseke+ ndi Tirasi.+

  • Genesis 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.+

  • Yesaya 66:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Ndidzachita zinthu zazikulu pakati pawo monga chizindikiro.+ Opulumuka ena ndidzawatumiza ku mitundu ya anthu,+ ku Tarisi,+ ku Puli, ndi ku Ludi.+ Ndidzawatumiza kwa anthu odziwa kukoka uta ku Tubala ndi ku Yavani.+ Ndidzawatumiza kuzilumba zakutali,+ kwa anthu amene sanamve mbiri yanga kapena kuona ulemerero wanga.+ Iwo adzanenadi za ulemerero wanga pakati pa mitundu ya anthu.+

  • Danieli 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+

  • Zekariya 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yuda ndidzamupinda kuti akhale uta wanga. Efuraimu ndidzamuika pa uta umenewo ngati muvi. Iwe Ziyoni, ine ndidzadzutsa ana ako+ kuti aukire ana a Girisi.+ Ndipo ndidzakusandutsa lupanga la munthu wamphamvu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena