Danieli 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mfumuyo idzakula mphamvu koma osati mwa iyo yokha.+ Idzawononga zinthu zambiri+ ndipo chilichonse chimene izidzachita chidzaiyendera bwino. Idzawononga anthu amphamvu ndi anthu oyera.+ Mateyu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+ Chivumbulutso 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zikamaliza kuchitira umboni wawo, chilombo chotuluka muphompho+ chidzachita nazo nkhondo, ndipo chidzazigonjetsa ndi kuzipha.+
24 Mfumuyo idzakula mphamvu koma osati mwa iyo yokha.+ Idzawononga zinthu zambiri+ ndipo chilichonse chimene izidzachita chidzaiyendera bwino. Idzawononga anthu amphamvu ndi anthu oyera.+
9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+
7 Zikamaliza kuchitira umboni wawo, chilombo chotuluka muphompho+ chidzachita nazo nkhondo, ndipo chidzazigonjetsa ndi kuzipha.+