Ezekieli 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wamkulu dzina lake anali Ohola, wamng’ono anali Oholiba. Akazi amenewa anakhala anga+ ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi.+ Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu.+ Ezekieli 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Mng’ono wake Oholiba ataona zimenezi,+ anayamba kukonda chiwerewere chodziwononga nacho kuposa mkulu wake. Anayamba kuchita uhule kuposa dama la mkulu wake.+
4 Wamkulu dzina lake anali Ohola, wamng’ono anali Oholiba. Akazi amenewa anakhala anga+ ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi.+ Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu.+
11 “Mng’ono wake Oholiba ataona zimenezi,+ anayamba kukonda chiwerewere chodziwononga nacho kuposa mkulu wake. Anayamba kuchita uhule kuposa dama la mkulu wake.+