Yesaya 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachite mantha, nyongolotsi iwe+ Yakobo, inuyo amuna a Isiraeli.+ Ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli. Mika 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo,+ ndipo ndinakuwombolani m’nyumba ya akapolo.+ Ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+
14 “Usachite mantha, nyongolotsi iwe+ Yakobo, inuyo amuna a Isiraeli.+ Ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli.
4 Ine ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo,+ ndipo ndinakuwombolani m’nyumba ya akapolo.+ Ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+