Salimo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+ Yesaya 43:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzawatumiza ku Babulo. Ndidzachititsa kuti zitsulo za ndende zimasuke+ ndiponso ndidzagonjetsa Akasidi amene ali m’zombo ndi kuwachititsa kulira mokuwa.+ Yesaya 47:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pali amene akutiwombola.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ Woyera wa Isiraeli.”+
14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+
14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzawatumiza ku Babulo. Ndidzachititsa kuti zitsulo za ndende zimasuke+ ndiponso ndidzagonjetsa Akasidi amene ali m’zombo ndi kuwachititsa kulira mokuwa.+