Levitiko 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “‘Ndidzaika mantha m’mitima ya otsala pakati panu+ amene ali m’dziko la adani awo, moti adzathawa m’tswatswa wa tsamba louluka, ndipo adzathawa ngati kuti akuthawa lupanga. Pamenepo adzagwa popanda munthu wowathamangitsa.+ Maliro 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Otithamangitsawo ndi aliwiro kuposa ziwombankhanga zouluka m’mwamba.+Iwo atithamangitsa pamapiri.+ Atibisalira m’chipululu.+
36 “‘Ndidzaika mantha m’mitima ya otsala pakati panu+ amene ali m’dziko la adani awo, moti adzathawa m’tswatswa wa tsamba louluka, ndipo adzathawa ngati kuti akuthawa lupanga. Pamenepo adzagwa popanda munthu wowathamangitsa.+
19 Otithamangitsawo ndi aliwiro kuposa ziwombankhanga zouluka m’mwamba.+Iwo atithamangitsa pamapiri.+ Atibisalira m’chipululu.+