Yeremiya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo ndidzawombanitsa munthu ndi mnzake, abambo ndi ana awo pa nthawi imodzi,”+ watero Yehova. “Sindidzawachitira chifundo kapena kuwamvera chisoni. Ndithu sindidzakhala ndi chifundo choti ndisawawononge.”’+ Ezekieli 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero inenso diso langa silimva chisoni+ ndipo sindichita chifundo.+ Ndiwabwezera mogwirizana ndi njira zawo.”+ Aroma 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+
14 Ndipo ndidzawombanitsa munthu ndi mnzake, abambo ndi ana awo pa nthawi imodzi,”+ watero Yehova. “Sindidzawachitira chifundo kapena kuwamvera chisoni. Ndithu sindidzakhala ndi chifundo choti ndisawawononge.”’+
10 Chotero inenso diso langa silimva chisoni+ ndipo sindichita chifundo.+ Ndiwabwezera mogwirizana ndi njira zawo.”+
18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+