Maliro 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda+ wam’mawa.Khuthula+ mtima wako pamaso+ pa Yehova ngati madzi.Pemphera utakweza manja+ ako kwa iye chifukwa cha ana ako,Amene akukomoka ndi njala m’misewu.+
19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda+ wam’mawa.Khuthula+ mtima wako pamaso+ pa Yehova ngati madzi.Pemphera utakweza manja+ ako kwa iye chifukwa cha ana ako,Amene akukomoka ndi njala m’misewu.+