1 Mafumu 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+ 2 Mafumu 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pambuyo pake mfumu ya Asuri+ inatenga Aisiraeli n’kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala,+ ndi ku Habori+ pafupi ndi mtsinje wa Gozani, ndiponso m’mizinda ya Amedi.+
34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+
11 Pambuyo pake mfumu ya Asuri+ inatenga Aisiraeli n’kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala,+ ndi ku Habori+ pafupi ndi mtsinje wa Gozani, ndiponso m’mizinda ya Amedi.+