2 Mafumu 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa nthawi imeneyo, atumiki a Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu n’kuzungulira mzindawo.+ 2 Mafumu 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gulu lankhondo la Akasidi+ linayamba kuthamangitsa mfumuyo ndipo linaipeza+ m’chipululu cha Yeriko.+ Pamenepo gulu lonse lankhondo la mfumuyo linabalalika n’kuisiya yokha. Yeremiya 52:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ziwerengero za anthu amene Nebukadirezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi izi: m’chaka cha 7 cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023.+
10 Pa nthawi imeneyo, atumiki a Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu n’kuzungulira mzindawo.+
5 Gulu lankhondo la Akasidi+ linayamba kuthamangitsa mfumuyo ndipo linaipeza+ m’chipululu cha Yeriko.+ Pamenepo gulu lonse lankhondo la mfumuyo linabalalika n’kuisiya yokha.
28 Ziwerengero za anthu amene Nebukadirezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi izi: m’chaka cha 7 cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023.+