Salimo 126:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyo tinaseka kwambiri,+Ndipo lilime lathu linatulutsa mawu okondwa.+Pamenepo anthu a mitundu ina anayamba kuuzana kuti:+“Yehova wachitira anthu amenewa zinthu zazikulu.”+ Yesaya 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezeka,+ koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona mmene mukudziperekera kwa anthu anu, ndipo adzachita manyazi.+ Ndithu, moto+ wanu udzanyeketsa adani anu. Yesaya 66:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Popeza ndikudziwa ntchito zawo+ ndi maganizo awo,+ ine ndikubwera kudzasonkhanitsa pamodzi mitundu yonse ndi zilankhulo zonse za anthu,+ ndipo iwo adzabwera n’kuona ulemerero wanga.”+
2 Pa nthawiyo tinaseka kwambiri,+Ndipo lilime lathu linatulutsa mawu okondwa.+Pamenepo anthu a mitundu ina anayamba kuuzana kuti:+“Yehova wachitira anthu amenewa zinthu zazikulu.”+
11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezeka,+ koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona mmene mukudziperekera kwa anthu anu, ndipo adzachita manyazi.+ Ndithu, moto+ wanu udzanyeketsa adani anu.
18 “Popeza ndikudziwa ntchito zawo+ ndi maganizo awo,+ ine ndikubwera kudzasonkhanitsa pamodzi mitundu yonse ndi zilankhulo zonse za anthu,+ ndipo iwo adzabwera n’kuona ulemerero wanga.”+