1 Mafumu 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako anagula phiri la Samariya* kwa Semeri ndi matalente* awiri a siliva. Ndiyeno anayamba kumanga mzinda paphiripo n’kuutcha dzina la Semeri mbuye wa phirilo, loti Samariya.+ Amosi 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’
24 Kenako anagula phiri la Samariya* kwa Semeri ndi matalente* awiri a siliva. Ndiyeno anayamba kumanga mzinda paphiripo n’kuutcha dzina la Semeri mbuye wa phirilo, loti Samariya.+
4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’