Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 13:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kodi zoona mukundinyozetsa pamaso pa anthu anga chifukwa cha balere wongodzaza m’manja ndi nyenyeswa za mkate?+ Kodi mukuphadi anthu osayenera kufa,+ ndipo mukusiya anthu osayenera kukhala ndi moyo, ponamiza anthu anga amene akumva bodza lanulo?”’+

  • Ezekieli 34:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, losera zoipa zimene zidzachitikire abusa a Isiraeli. Losera, ndipo uuze abusawo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka abusa a Isiraeli,+ amene akungodzidyetsa okha!+ Kodi abusa ntchito yawo si kudyetsa nkhosa?+

  • Mateyu 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+

  • Aroma 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pakuti anthu oterowo si akapolo a Ambuye wathu Khristu, koma a mimba zawo.+ Ndipo mwa kulankhula mawu okopa+ ndi achinyengo+ amanyenga anthu oona mtima.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena