Salimo 77:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mitambo yatulutsa mabingu ndi kugwetsa madzi.+Thambo latulutsa mkokomo.Mphezi zanu zinawala paliponse ngati mivi.+ Salimo 77:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+ Salimo 144:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ng’animitsani mphezi kuti muwabalalitse.+Tumizani mivi yanu kuti muwasokoneze.+
17 Mitambo yatulutsa mabingu ndi kugwetsa madzi.+Thambo latulutsa mkokomo.Mphezi zanu zinawala paliponse ngati mivi.+
18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+