Yeremiya 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Tsoka amene akumanga nyumba yake+ komanso zipinda zake zam’mwamba mopanda chilungamo mwa kugwiritsa ntchito anthu kwaulere, osawapatsa malipiro.+ Ezekieli 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Tsoka mzinda wokhetsa magazi!+ Ine ndidzaunjika mulu waukulu wa nkhuni.+ Nahumu 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsoka mzinda wokhetsa magazi.+ Mzindawo wadzaza ndi chinyengo ndi chifwamba, moti nthawi zonse umafunkha zinthu za anthu ena. Chivumbulutso 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo ndinaona kuti mkaziyo anali ataledzera ndi magazi+ a oyera, ndiponso magazi a mboni za Yesu.+ Nditamuona mkaziyo, ndinadabwa kwambiri.+
13 “Tsoka amene akumanga nyumba yake+ komanso zipinda zake zam’mwamba mopanda chilungamo mwa kugwiritsa ntchito anthu kwaulere, osawapatsa malipiro.+
9 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Tsoka mzinda wokhetsa magazi!+ Ine ndidzaunjika mulu waukulu wa nkhuni.+
3 Tsoka mzinda wokhetsa magazi.+ Mzindawo wadzaza ndi chinyengo ndi chifwamba, moti nthawi zonse umafunkha zinthu za anthu ena.
6 Ndipo ndinaona kuti mkaziyo anali ataledzera ndi magazi+ a oyera, ndiponso magazi a mboni za Yesu.+ Nditamuona mkaziyo, ndinadabwa kwambiri.+