Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kumbukirani Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli atumiki anu, amene munawalumbirira pa inu mwini,+ powauza kuti, ‘Ndidzachulukitsa mbewu yanu ngati nyenyezi zakumwamba,+ ndipo dziko lonseli limene ndalipatula ndidzalipereka kwa mbewu yanu,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale.’”+

  • Yeremiya 31:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Kodi Efuraimu si mwana wanga wamtengo wapatali, kapena mwana wanga wokondedwa?+ Pamlingo umene ndalankhula zomulanga, ndidzakumbukira kumuchitira zabwino pamlingo womwewo.+ N’chifukwa chake m’mimba mwanga mukubwadamuka chifukwa cha iye.+ Mosalephera ndidzamumvera chisoni,”+ watero Yehova.

  • Maliro 3:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ngakhale kuti watichititsa kumva chisoni,+ ndithu adzatichitira chifundo chifukwa kukoma mtima kwake kosatha n’kwakukulu.+

  • Mateyu 24:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kunena zoona, masikuwo akanapanda kufupikitsidwa, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwawo,+ masikuwo adzafupikitsidwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena