Yesaya 63:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anati: “Ndithu awa ndi anthu anga,+ ana amene sadzachita zachinyengo.”+ Choncho iye anakhala Mpulumutsi wawo.+ Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+ Akolose 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamanamizane.+ Vulani umunthu+ wakale pamodzi ndi ntchito zake, Chivumbulutso 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’kamwa mwawo simunapezeke chinyengo,+ ndipo alibe chilema.+ Chivumbulutso 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma chilichonse chosapatulika, ndi aliyense wochita zonyansa+ ndiponso wabodza,+ sadzalowa mumzindawo.+ Amene adzalowemo ndi okhawo olembedwa mumpukutu wa moyo, umene ndi wa Mwanawankhosa.+
8 Iye anati: “Ndithu awa ndi anthu anga,+ ana amene sadzachita zachinyengo.”+ Choncho iye anakhala Mpulumutsi wawo.+
25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+
27 Koma chilichonse chosapatulika, ndi aliyense wochita zonyansa+ ndiponso wabodza,+ sadzalowa mumzindawo.+ Amene adzalowemo ndi okhawo olembedwa mumpukutu wa moyo, umene ndi wa Mwanawankhosa.+