Yesaya 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mizinda ya Aroweri+ imene yasiyidwa m’mbuyo yangosanduka malo okhala ziweto, kumene ziwetozo zimagona pansi popanda woziopsa.+ Ezekieli 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mzinda wa Raba+ ndidzausandutsa malo odyetserako ngamila, ndipo dziko la ana a Amoni ndidzalisandutsa malo opumulirako gulu la nkhosa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+
2 Mizinda ya Aroweri+ imene yasiyidwa m’mbuyo yangosanduka malo okhala ziweto, kumene ziwetozo zimagona pansi popanda woziopsa.+
5 Mzinda wa Raba+ ndidzausandutsa malo odyetserako ngamila, ndipo dziko la ana a Amoni ndidzalisandutsa malo opumulirako gulu la nkhosa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+